Ezekieli 29:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho, iwe ndikulanga ndi kuwononga ngalande zako zotuluka mu Nailo.+ Dziko la Iguputo ndiliwononga. Ndilisandutsa malo ouma komanso bwinja,+ kuchokera ku Migidoli+ mpaka ku Seyene+ kukafika kumalire a dziko la Itiyopiya.
10 Choncho, iwe ndikulanga ndi kuwononga ngalande zako zotuluka mu Nailo.+ Dziko la Iguputo ndiliwononga. Ndilisandutsa malo ouma komanso bwinja,+ kuchokera ku Migidoli+ mpaka ku Seyene+ kukafika kumalire a dziko la Itiyopiya.