Ezekieli 29:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho, iwe ndikulanga ndipo ndiwononga mtsinje wako wa Nailo ndipo dziko la Iguputo ndiliwononga nʼkulisandutsa malo ouma komanso bwinja,+ kuchokera ku Migidoli+ mpaka ku Seyene+ nʼkukafika kumalire a dziko la Itiyopiya.
10 Choncho, iwe ndikulanga ndipo ndiwononga mtsinje wako wa Nailo ndipo dziko la Iguputo ndiliwononga nʼkulisandutsa malo ouma komanso bwinja,+ kuchokera ku Migidoli+ mpaka ku Seyene+ nʼkukafika kumalire a dziko la Itiyopiya.