Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 44:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndiyeno amuna onse amene anali kudziwa kuti akazi awo anali kupereka nsembe zautsi kwa milungu ina,+ akazi onse amene anaimirira ndi kupanga mpingo waukulu, komanso anthu onse amene anali kukhala ku Iguputo+ m’dera la Patirosi,+ anayankha Yeremiya kuti:

  • Ezekieli 29:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndidzabwezeretsa gulu la Aiguputo amene anagwidwa n’kupita nawo kudziko lina. Ndidzawabwezeretsa kudera la Patirosi,+ m’dziko limene anachokera. Kumeneko adzakhazikitsa ufumu wonyozeka.

  • Ezekieli 30:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Mzinda wa Patirosi+ ndidzausandutsa bwinja. Mzinda wa Zowani+ ndidzautentha ndi moto ndipo ndidzapereka ziweruzo mumzinda wa No.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena