Genesis 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Patirusimu+ ndi Kasiluhimu+ (Afilisiti+ anachokera mwa iyeyu), ndiponso Kafitorimu.+ 1 Mbiri 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Patirusimu,+ ndi Kasiluhimu+ (Afilisiti+ anachokera mwa iyeyu), ndiponso Kafitorimu.+ Ezekieli 30:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mzinda wa Patirosi+ ndidzausandutsa bwinja. Mzinda wa Zowani+ ndidzautentha ndi moto ndipo ndidzapereka ziweruzo mumzinda wa No.+
14 Mzinda wa Patirosi+ ndidzausandutsa bwinja. Mzinda wa Zowani+ ndidzautentha ndi moto ndipo ndidzapereka ziweruzo mumzinda wa No.+