Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 43:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kenako ukawauze kuti, ‘Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Inetu ndikuitana Nebukadirezara mfumu ya Babulo+ mtumiki wanga,+ ndipo ndidzaika mpando wake wachifumu pamwamba penipeni pa miyala iyi imene ndaibisa. Iye adzamanga hema wake waulemerero pamwamba pa miyala imeneyi.

  • Ezekieli 29:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 “Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ine ndipereka dziko la Iguputo kwa Nebukadirezara mfumu ya Babulo.+ Adzatenga chuma chake chochuluka ndi kulanda zinthu zake zambiri.+ Zimenezi zidzakhala malipiro a gulu lake lankhondo.’

  • Ezekieli 30:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ndidzawononga khamu la ku Iguputo pogwiritsa ntchito dzanja la Nebukadirezara, mfumu ya Babulo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena