Ezekieli 29:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ine ndipereka dziko la Iguputo kwa Nebukadirezara mfumu ya Babulo.+ Adzatenga chuma chake chochuluka ndi kulanda zinthu zake zambiri.+ Zimenezi zidzakhala malipiro a gulu lake lankhondo.’ Ezekieli 32:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Lupanga la mfumu ya Babulo lidzafika pa iwe.+
19 “Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ine ndipereka dziko la Iguputo kwa Nebukadirezara mfumu ya Babulo.+ Adzatenga chuma chake chochuluka ndi kulanda zinthu zake zambiri.+ Zimenezi zidzakhala malipiro a gulu lake lankhondo.’