Ezekieli 32:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndidzachititsa khamu la anthu ako kuphedwa ndi malupanga a anthu amphamvu. Anthu onsewo ndi olamulira ankhanza a mitundu ina ya anthu.+ Iwo adzawononga zonse zimene Iguputo amazinyadira ndipo khamu lake lonse lidzawonongedwa.+
12 Ndidzachititsa khamu la anthu ako kuphedwa ndi malupanga a anthu amphamvu. Anthu onsewo ndi olamulira ankhanza a mitundu ina ya anthu.+ Iwo adzawononga zonse zimene Iguputo amazinyadira ndipo khamu lake lonse lidzawonongedwa.+