Yeremiya 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ngakhale anthu a ku Nofi+ ndi ku Tahapanesi+ anawononga dziko lako.*+ Ezekieli 30:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mumzinda wa Tahapanesi+ mudzagwa mdima masana ndikadzathyola magoli a Iguputo kumeneko.+ Mphamvu zimene amazinyadira zidzathetsedwa.+ Iye adzakutidwa ndi mitambo+ ndipo anthu a m’mizinda yake yozungulira adzatengedwa kupita ku ukapolo.+
18 Mumzinda wa Tahapanesi+ mudzagwa mdima masana ndikadzathyola magoli a Iguputo kumeneko.+ Mphamvu zimene amazinyadira zidzathetsedwa.+ Iye adzakutidwa ndi mitambo+ ndipo anthu a m’mizinda yake yozungulira adzatengedwa kupita ku ukapolo.+