-
Ezekieli 31:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 “‘Kodi iwe ukufanana ndi ndani pa nkhani ya ulemerero+ ndi kukula pakati pa mitengo ya mu Edeni?+ Koma ndithu udzatsikira pansi pa nthaka limodzi ndi mitengo ya mu Edeni.+ Udzagona pakati pa anthu osadulidwa limodzi ndi ophedwa ndi lupanga. Mtengo umenewu ukuimira Farao ndi khamu lake lonse,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
-