Ezekieli 31:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mtengo umenewu ndinaukongoletsa pouchulukitsira nthambi zamasamba ambiri.+ Mitengo ina yonse ya mu Edeni, imene inali m’munda wa Mulungu woona, inali kuuchitira nsanje.’+
9 Mtengo umenewu ndinaukongoletsa pouchulukitsira nthambi zamasamba ambiri.+ Mitengo ina yonse ya mu Edeni, imene inali m’munda wa Mulungu woona, inali kuuchitira nsanje.’+