Danieli 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Masamba ake anali okongola ndipo unali ndi zipatso zambiri. Mumtengomo munali zakudya zokwanira chamoyo chilichonse. Nyama zakutchire zinali kukhala pansi pake.+ Mbalame zam’mlengalenga zinali kukhala panthambi zake.
21 Masamba ake anali okongola ndipo unali ndi zipatso zambiri. Mumtengomo munali zakudya zokwanira chamoyo chilichonse. Nyama zakutchire zinali kukhala pansi pake.+ Mbalame zam’mlengalenga zinali kukhala panthambi zake.