-
Yeremiya 46:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Iguputo ali ngati ngʼombe yaikazi yooneka bwino imene sinaberekepo,
Koma ntchentche zoluma zidzabwera kuchokera kumpoto kudzamuwononga.
-