Yeremiya 46:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iguputo ndi ng’ombe yaikazi yokongola kwambiri imene sinaberekepo. Udzudzu wovutitsa ndi wowononga wochokera kumpoto udzabwera kuti umuwononge.+
20 Iguputo ndi ng’ombe yaikazi yokongola kwambiri imene sinaberekepo. Udzudzu wovutitsa ndi wowononga wochokera kumpoto udzabwera kuti umuwononge.+