Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 19:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Akalonga a ku Zowani achita zopusa.+ Akalonga a ku Nofi+ anyengezedwa. Atsogoleri+ a mafuko achititsa Iguputo kuyenda uku ndi uku.

  • Yeremiya 44:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Mulungu anauza Yeremiya uthenga woti akauze Ayuda onse amene anali kukhala m’dziko la Iguputo,+ m’madera a Migidoli,+ Tahapanesi,+ Nofi+ ndi Patirosi.+ Uthengawo unali wakuti:

  • Yeremiya 46:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 ‘Longedza katundu wopita naye ku ukapolo,+ iwe mwana wamkazi wokhala+ mu Iguputo. Pakuti mzinda wa Nofi+ udzakhala chinthu chodabwitsa ndipo adzautentha, moti simudzapezeka aliyense wokhalamo.+

  • Ezekieli 30:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ndidzawononganso mafano onyansa+ ndi kuthetsa milungu yopanda pake ku Nofi.+ Sipadzapezekanso mtsogoleri wochokera m’dziko la Iguputo, ndipo ndidzachititsa anthu a m’dzikolo kukhala mwamantha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena