Hoseya 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ngakhale kuti inu Aisiraeli mukuchita dama,+ Yuda asakhale wolakwa+ ndipo anthu inu musabwere ku Giligala.+ Musapitenso ku Beti-aveni+ kapena kulumbira kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo!’+ Hoseya 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Ku Giliyadi anthu akuchita zamatsenga+ ndiponso akulankhula zabodza.+ Ku Giligala akupereka nsembe ng’ombe zamphongo.+ Komanso maguwa awo ansembe ali ngati milu ya miyala m’mizere ya m’munda.+ Amosi 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Musakhale ndi mtima wofuna kupita ku Beteli+ ndipo musabwere ku Giligala.+ Musadutse malire kupita ku Beere-seba+ chifukwa ndithu Giligala adzagwidwa ndi kutengedwa kupita ku ukapolo+ ndipo Beteli adzakhala malo ochitikira zinthu zamatsenga.+
15 Ngakhale kuti inu Aisiraeli mukuchita dama,+ Yuda asakhale wolakwa+ ndipo anthu inu musabwere ku Giligala.+ Musapitenso ku Beti-aveni+ kapena kulumbira kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo!’+
11 “Ku Giliyadi anthu akuchita zamatsenga+ ndiponso akulankhula zabodza.+ Ku Giligala akupereka nsembe ng’ombe zamphongo.+ Komanso maguwa awo ansembe ali ngati milu ya miyala m’mizere ya m’munda.+
5 Musakhale ndi mtima wofuna kupita ku Beteli+ ndipo musabwere ku Giligala.+ Musadutse malire kupita ku Beere-seba+ chifukwa ndithu Giligala adzagwidwa ndi kutengedwa kupita ku ukapolo+ ndipo Beteli adzakhala malo ochitikira zinthu zamatsenga.+