Hoseya 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ku Giliyadi anthu akuchita zachinyengo*+ ndiponso akulankhula mabodza. Ku Giligala, akupereka nsembe ngʼombe zamphongo.+Ndipo maguwa awo ansembe ali ngati milu yamiyala mʼmunda.+
11 Ku Giliyadi anthu akuchita zachinyengo*+ ndiponso akulankhula mabodza. Ku Giligala, akupereka nsembe ngʼombe zamphongo.+Ndipo maguwa awo ansembe ali ngati milu yamiyala mʼmunda.+