Deuteronomo 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 mtima wanu n’kuyamba kudzikweza+ ndi kuiwala Yehova Mulungu wanu amene anakutulutsani m’dziko la Iguputo, m’nyumba yaukapolo.+ Deuteronomo 32:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yesuruni*+ atayamba kunenepa, anayamba kupanduka.+Iwe wanenepa, wakulupala, wakhuta mopitirira muyezo.+Pamenepo iye anasiya Mulungu amene anam’panga,+Ndi kunyoza Thanthwe+ la chipulumutso chake. 2 Mbiri 26:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma atangokhala wamphamvu, mtima wake unadzikuza+ mpaka kufika pom’pweteketsa.+ Choncho anachita zosakhulupirika kwa Yehova Mulungu wake ndipo anapita m’kachisi wa Yehova kukafukiza paguwa lansembe zofukiza.+ Miyambo 30:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 kuti ndisakhute kwambiri n’kukukanani+ kuti: “Kodi Yehova ndani?”+ ndiponso kuti ndisasauke n’kukaba ndi kunyozetsa dzina la Mulungu wanga.+
14 mtima wanu n’kuyamba kudzikweza+ ndi kuiwala Yehova Mulungu wanu amene anakutulutsani m’dziko la Iguputo, m’nyumba yaukapolo.+
15 Yesuruni*+ atayamba kunenepa, anayamba kupanduka.+Iwe wanenepa, wakulupala, wakhuta mopitirira muyezo.+Pamenepo iye anasiya Mulungu amene anam’panga,+Ndi kunyoza Thanthwe+ la chipulumutso chake.
16 Koma atangokhala wamphamvu, mtima wake unadzikuza+ mpaka kufika pom’pweteketsa.+ Choncho anachita zosakhulupirika kwa Yehova Mulungu wake ndipo anapita m’kachisi wa Yehova kukafukiza paguwa lansembe zofukiza.+
9 kuti ndisakhute kwambiri n’kukukanani+ kuti: “Kodi Yehova ndani?”+ ndiponso kuti ndisasauke n’kukaba ndi kunyozetsa dzina la Mulungu wanga.+