Numeri 1:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Pa nthawi yosamutsa chihema chopatulika, Aleviwo azichipasula,+ ndipo mukafika pomanga msasa, iwo ndiwo azimanga chihemacho. Aliyense amene si Mlevi akayandikira chihemacho aziphedwa.+
51 Pa nthawi yosamutsa chihema chopatulika, Aleviwo azichipasula,+ ndipo mukafika pomanga msasa, iwo ndiwo azimanga chihemacho. Aliyense amene si Mlevi akayandikira chihemacho aziphedwa.+