2 Mbiri 26:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma atangokhala wamphamvu, mtima wake unayamba kudzikuza mpaka kufika pomʼpweteketsa. Iye anachita zosakhulupirika kwa Yehova Mulungu wake ndipo anapita mʼkachisi wa Yehova kukapereka nsembe zofukiza paguwa lansembe.+
16 Koma atangokhala wamphamvu, mtima wake unayamba kudzikuza mpaka kufika pomʼpweteketsa. Iye anachita zosakhulupirika kwa Yehova Mulungu wake ndipo anapita mʼkachisi wa Yehova kukapereka nsembe zofukiza paguwa lansembe.+