Ekisodo 34:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti simuyenera kugwadira mulungu wina,+ chifukwa Yehova, amene dzina lake ndi Nsanje, alidi Mulungu wansanje.*+ Deuteronomo 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi moto wowononga,+ iye ndi Mulungu wofuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha basi.*+ Salimo 78:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Iwo anapitiriza kumukhumudwitsa ndi malo awo okwezeka,+Ndipo anamuchititsa nsanje ndi zifaniziro zawo zogoba.+ Yesaya 65:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ndatambasula manja anga tsiku lonse kwa anthu amakani,*+ amene akuyenda m’njira yoipa+ potsatira maganizo awo,+ 1 Akorinto 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kapena “kodi tikufuna kuputa nsanje+ ya Yehova”? Kodi mphamvu zathu zingafanane ndi zake?+
14 Pakuti simuyenera kugwadira mulungu wina,+ chifukwa Yehova, amene dzina lake ndi Nsanje, alidi Mulungu wansanje.*+
24 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi moto wowononga,+ iye ndi Mulungu wofuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha basi.*+
58 Iwo anapitiriza kumukhumudwitsa ndi malo awo okwezeka,+Ndipo anamuchititsa nsanje ndi zifaniziro zawo zogoba.+
2 “Ndatambasula manja anga tsiku lonse kwa anthu amakani,*+ amene akuyenda m’njira yoipa+ potsatira maganizo awo,+