Oweruza 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ana a Isiraeli anayamba kulirira Yehova,+ chifukwa Yabini anawapondereza+ kwambiri zaka 20, ndipo iye anali ndi magaleta ankhondo 900 okhala ndi zitsulo zazitali zakuthwa m’mawilo.+ 1 Samueli 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo m’dziko lonse la Isiraeli munalibe wosula zitsulo. Izi zinali choncho chifukwa Afilisiti anati: “Aheberi asasule lupanga kapena mkondo.”+
3 Ana a Isiraeli anayamba kulirira Yehova,+ chifukwa Yabini anawapondereza+ kwambiri zaka 20, ndipo iye anali ndi magaleta ankhondo 900 okhala ndi zitsulo zazitali zakuthwa m’mawilo.+
19 Ndipo m’dziko lonse la Isiraeli munalibe wosula zitsulo. Izi zinali choncho chifukwa Afilisiti anati: “Aheberi asasule lupanga kapena mkondo.”+