Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 2:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Zikatero, Yehova anali kuwapatsa oweruza,+ ndipo anali kuwapulumutsa m’manja mwa ofunkha.+

  • Oweruza 10:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Asidoni,+ Aamaleki+ ndi Amidiyani+ atakuponderezani,+ sindinakupulumutseni m’manja mwawo mutafuulira kwa ine?

  • 1 Samueli 12:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pamenepo Yehova anatumiza Yerubaala,+ Bedani, Yefita+ ndi Samueli+ ndipo anakulanditsani m’manja mwa adani anu onse okuzungulirani, kuti mukhale popanda chokuopsani.+

  • Nehemiya 9:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Chifukwa chochita zimenezi, munawapereka m’manja mwa adani awo+ amene anapitiriza kuwasautsa.+ Koma akakumana ndi nsautso, anali kukulirirani,+ ndipo inu munali kumva muli kumwambako.+ Chifukwa cha chifundo chanu chachikulu,+ munali kuwapatsa owapulumutsa+ amene anali kuwalanditsa m’manja mwa adani awo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena