Oweruza 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo ana a Isiraeli anayamba kufuulira Yehova kuti awathandize.+ Pamenepo Yehova anapereka mpulumutsi+ wa ana a Isiraeli kuti awapulumutse. Ameneyu anali Otiniyeli,+ mwana wamwamuna wa Kenazi,+ mng’ono wake wa Kalebe.+ 1 Samueli 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Yehova anatumiza Yerubaala,+ Bedani, Yefita+ ndi Samueli+ ndipo anakulanditsani m’manja mwa adani anu onse okuzungulirani, kuti mukhale popanda chokuopsani.+
9 Ndipo ana a Isiraeli anayamba kufuulira Yehova kuti awathandize.+ Pamenepo Yehova anapereka mpulumutsi+ wa ana a Isiraeli kuti awapulumutse. Ameneyu anali Otiniyeli,+ mwana wamwamuna wa Kenazi,+ mng’ono wake wa Kalebe.+
11 Pamenepo Yehova anatumiza Yerubaala,+ Bedani, Yefita+ ndi Samueli+ ndipo anakulanditsani m’manja mwa adani anu onse okuzungulirani, kuti mukhale popanda chokuopsani.+