Oweruza 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo mkwiyo wa Yehova unayakira Isiraeli,+ moti anawapereka m’manja mwa ofunkha, ndipo anayamba kufunkha zinthu zawo.+ Iye anawagulitsa kwa adani awo owazungulira+ moti sanathe kuima pamaso pa adani awo.+ 2 Mbiri 36:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho anawabweretsera mfumu ya Akasidi+ yomwe inapha anyamata awo ndi lupanga+ m’nyumba yopatulika.+ Sinachitire chisoni mnyamata kapena namwali, wachikulire kapena nkhalamba yotheratu.+ Mulungu anapereka zonse m’manja mwake. Salimo 106:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Mobwerezabwereza anali kuwapereka m’manja mwa anthu a mitundu ina,+Kuti anthu odana nawo awalamulire,+
14 Pamenepo mkwiyo wa Yehova unayakira Isiraeli,+ moti anawapereka m’manja mwa ofunkha, ndipo anayamba kufunkha zinthu zawo.+ Iye anawagulitsa kwa adani awo owazungulira+ moti sanathe kuima pamaso pa adani awo.+
17 Choncho anawabweretsera mfumu ya Akasidi+ yomwe inapha anyamata awo ndi lupanga+ m’nyumba yopatulika.+ Sinachitire chisoni mnyamata kapena namwali, wachikulire kapena nkhalamba yotheratu.+ Mulungu anapereka zonse m’manja mwake.
41 Mobwerezabwereza anali kuwapereka m’manja mwa anthu a mitundu ina,+Kuti anthu odana nawo awalamulire,+