Levitiko 26:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Iwo adzagwetsana okhaokha ngati kuti akuthawa lupanga, koma popanda munthu wowathamangitsa. Simudzatha n’komwe kulimbana ndi adani anu.+ Deuteronomo 28:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yehova adzakuchititsani kuti mugonje pamaso pa adani anu.+ Pokamenyana nawo nkhondo mudzadutsa njira imodzi, koma pothawa pamaso pawo mudzadutsa njira 7. Mudzakhala chinthu chonyansa kwa mafumu onse a dziko lapansi.+
37 Iwo adzagwetsana okhaokha ngati kuti akuthawa lupanga, koma popanda munthu wowathamangitsa. Simudzatha n’komwe kulimbana ndi adani anu.+
25 Yehova adzakuchititsani kuti mugonje pamaso pa adani anu.+ Pokamenyana nawo nkhondo mudzadutsa njira imodzi, koma pothawa pamaso pawo mudzadutsa njira 7. Mudzakhala chinthu chonyansa kwa mafumu onse a dziko lapansi.+