Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 7:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ana a Isiraeli sadzathanso kulimbana ndi adani awo.+ Iwo azingothawa kwa adani awo, chifukwa iwonso akhala zinthu zoyenera kuwonongedwa. Sindidzakhalanso nanu kufikira mutachotsa pakati panu zinthu zoyenera kuwonongedwazo.+

  • Oweruza 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pamenepo mkwiyo wa Yehova unayakira Isiraeli,+ moti anawapereka m’manja mwa ofunkha, ndipo anayamba kufunkha zinthu zawo.+ Iye anawagulitsa kwa adani awo owazungulira+ moti sanathe kuima pamaso pa adani awo.+

  • Yesaya 10:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Palibe chimene mudzachite, koma mudzagwada pakati pa akaidi ndiponso muzidzagwa pakati pa anthu amene aphedwa.+ Chifukwa cha zonsezi, mkwiyo wake sunabwerere, ndipo dzanja lake lidakali lotambasula.+

  • Yeremiya 37:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti ngakhale anthu inu mutapha gulu lonse lankhondo la Akasidi amene akumenyana nanu+ ndipo pangotsala amuna ovulala kwambiri pakati pawo,+ aliyense wa amenewo adzadzuka muhema wake ndi kubwera kudzatentha mzinda uno.”’”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena