Yesaya 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Palibe chimene mudzachite, koma mudzagwada pakati pa akaidiKapena mudzakhala mʼgulu la anthu ophedwa. Chifukwa cha zonsezi, mkwiyo wake sunabwerere,Koma dzanja lake lidakali lotambasula kuti awalange.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:4 Yesaya 1, ptsa. 134, 142-143
4 Palibe chimene mudzachite, koma mudzagwada pakati pa akaidiKapena mudzakhala mʼgulu la anthu ophedwa. Chifukwa cha zonsezi, mkwiyo wake sunabwerere,Koma dzanja lake lidakali lotambasula kuti awalange.+