Yesaya 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Palibe chimene mudzachite, koma mudzagwada pakati pa akaidi ndiponso muzidzagwa pakati pa anthu amene aphedwa.+ Chifukwa cha zonsezi, mkwiyo wake sunabwerere, ndipo dzanja lake lidakali lotambasula.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:4 Yesaya 1, ptsa. 134, 142-143
4 Palibe chimene mudzachite, koma mudzagwada pakati pa akaidi ndiponso muzidzagwa pakati pa anthu amene aphedwa.+ Chifukwa cha zonsezi, mkwiyo wake sunabwerere, ndipo dzanja lake lidakali lotambasula.+