Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 24:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndidzawasandutsa chinthu chimene maufumu onse a padziko lapansi adzanthunthumira nacho, chifukwa cha masoka aakulu amene ndidzawagwetsera.+ Anthu a mitundu ina adzawatonza, kuwayesa chosereula, kuwanyoza+ ndipo adzakhala otembereredwa+ kulikonse kumene ndidzawabalalitsirako.+

  • Yeremiya 29:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “‘Ndidzawathamangitsa ndi lupanga, njala yaikulu ndi mliri, ndipo ndidzawasandutsa chinthu chimene maufumu onse a padziko lapansi adzanthunthumira nacho.+ Ndidzawachititsa kukhala chinthu chotembereredwa, chodabwitsa, chochilizira mluzu ndiponso chotonzedwa pakati pa mitundu yonse ya anthu a kumene ndidzawabalalitsirako.+

  • Ezekieli 23:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Kudzabwera khamu la anthu kudzawaukira+ ndi kuwasandutsa chinthu chochititsa mantha komanso chinthu choyenera kutengedwa ndi adani.+

  • Luka 21:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Anthu adzaphedwa ndi lupanga ndiponso kutengedwa ukapolo kupita nawo ku mitundu ina yonse.+ Anthu a mitundu ina adzapondaponda Yerusalemu, kufikira nthawi zoikidwiratu+ za anthu a mitundu inawo zitakwanira.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena