Ekisodo 33:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma Mulungu anati: “Ineyo ndidzakuonetsa ubwino wanga wonse,+ ndipo ndidzalengeza dzina langa lakuti Yehova kwa iwe.+ Amene ndikufuna kum’komera mtima ndidzam’komera mtima, ndipo amene ndikufuna kum’sonyeza chifundo, ndidzam’sonyeza chifundo.”+ Salimo 27:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ngati ndikanakhala wopanda chikhulupiriro poona ubwino wa Yehova m’dziko la anthu amoyo, ndikanataya chiyembekezo.+
19 Koma Mulungu anati: “Ineyo ndidzakuonetsa ubwino wanga wonse,+ ndipo ndidzalengeza dzina langa lakuti Yehova kwa iwe.+ Amene ndikufuna kum’komera mtima ndidzam’komera mtima, ndipo amene ndikufuna kum’sonyeza chifundo, ndidzam’sonyeza chifundo.”+
13 Ngati ndikanakhala wopanda chikhulupiriro poona ubwino wa Yehova m’dziko la anthu amoyo, ndikanataya chiyembekezo.+