Mateyu 12:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Pa chifukwa chimenechi, ndikukuuzani kuti, Anthu adzakhululukidwa tchimo la mtundu uliwonse ndi mawu aliwonse onyoza, koma wonyoza mzimu sadzakhululukidwa.+ Luka 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo aliyense wonena mawu onyoza Mwana wa munthu, adzakhululukidwa. Koma wonyoza mzimu woyera sadzakhululukidwa.+
31 “Pa chifukwa chimenechi, ndikukuuzani kuti, Anthu adzakhululukidwa tchimo la mtundu uliwonse ndi mawu aliwonse onyoza, koma wonyoza mzimu sadzakhululukidwa.+
10 Ndipo aliyense wonena mawu onyoza Mwana wa munthu, adzakhululukidwa. Koma wonyoza mzimu woyera sadzakhululukidwa.+