Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Maliko 3:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Ndithu ndikukuuzani, ana a anthu adzakhululukidwa zinthu zonse, kaya ndi machimo otani amene anachita kapena mawu onyoza otani amene analankhula.+

  • Machitidwe 7:51
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 51 “Anthu okanika inu ndi osachita mdulidwe wa mumtima+ ndi m’makutu. Nthawi zonse mumatsutsana ndi mzimu woyera. Mmene anachitira makolo anu inunso mukuchita chimodzimodzi.+

  • Aheberi 6:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pali anthu amene Mulungu anawaunikira,+ amene analawa mphatso yaulere yakumwamba,+ amene analandira mzimu woyera,+

  • Aheberi 6:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 koma tsopano anagwa.+ Anthu amenewa n’zosatheka kuwadzutsanso kuti alape.+ N’zosatheka chifukwa chakuti anthu amenewa akupachika kachiwiri Mwana wa Mulungu ndi kumunyoza poyera.+

  • 1 Yohane 5:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ngati wina waona m’bale wake akuchita tchimo losabweretsa imfa,+ amupempherere, ndipo Mulungu adzamupatsa moyo.+ Panotu ndikunena za ochita machimo osabweretsa imfa.+ Koma palinso tchimo lobweretsa imfa. Ndipo sindikunena kuti mupempherere munthu amene wachita tchimo loterolo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena