Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 30:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mukabwerera+ kwa Yehova, abale anu ndi ana anu adzachitiridwa chifundo+ ndi anthu amene anawagwira n’kupita nawo kudziko lina. Chotero iwo adzaloledwa kubwerera kudziko lino+ chifukwa Yehova Mulungu wanu ndi wachisomo+ ndiponso wachifundo,+ ndipo sadzayang’ana kumbali mukabwerera kwa iye.”+

  • Ezara 7:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Iye wandisonyeza kukoma mtima kosatha+ pamaso pa mfumu, pamaso pa aphungu ake,+ ndi pamaso pa akalonga onse amphamvu a mfumu. Ineyo ndinadzilimbitsa chifukwa dzanja+ la Yehova Mulungu wanga linali pa ine, ndipo ndinasonkhanitsa atsogoleri a Aisiraeli kuti apite nane limodzi.

  • Nehemiya 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Komanso andipatse kalata yopita kwa Asafu amene akuyang’anira nkhalango ya mfumu, kuti akandipatse mitengo yokamangira zipata za Nyumba ya Chitetezo Champhamvu+ ya kukachisi,+ mpanda+ wa mzindawo ndiponso nyumba imene ndizikakhalamo.” Choncho mfumu inandipatsa makalatawo, chifukwa Mulungu anandikomera mtima.+

  • Salimo 106:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Ndipo anali kuchititsa kuti anthu onse owagwira ukapolo

      Awamvere chisoni.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena