Nehemiya 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero anandiuza kuti: “Anthu otsala amene ali m’chigawo,*+ amene anathawa ku ukapolo, ali pamavuto aakulu+ ndipo akunyozedwa.+ Nawonso mpanda+ wa Yerusalemu unagwa ndipo zipata+ zake zinatenthedwa ndi moto.” Nehemiya 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamapeto pake ndinawauza kuti: “Inu mukuona vuto lalikulu limene tili nalo. Mukuona kuti Yerusalemu ali bwinja ndipo zipata zake zinatenthedwa ndi moto. Tiyeni timange mpanda wa Yerusalemu kuti anthu asiye kutitonza.”+
3 Chotero anandiuza kuti: “Anthu otsala amene ali m’chigawo,*+ amene anathawa ku ukapolo, ali pamavuto aakulu+ ndipo akunyozedwa.+ Nawonso mpanda+ wa Yerusalemu unagwa ndipo zipata+ zake zinatenthedwa ndi moto.”
17 Pamapeto pake ndinawauza kuti: “Inu mukuona vuto lalikulu limene tili nalo. Mukuona kuti Yerusalemu ali bwinja ndipo zipata zake zinatenthedwa ndi moto. Tiyeni timange mpanda wa Yerusalemu kuti anthu asiye kutitonza.”+