Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 25:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kenako gulu lonse lankhondo la Akasidi, lomwe linali ndi mkulu wa asilikali olondera mfumu uja, linagwetsa mpanda wonse wa Yerusalemu.+

  • Nehemiya 2:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pamapeto pake ndinawauza kuti: “Inu mukuona vuto lalikulu limene tili nalo. Mukuona kuti Yerusalemu ali bwinja ndipo zipata zake zinatenthedwa ndi moto. Tiyeni timange mpanda wa Yerusalemu kuti anthu asiye kutitonza.”+

  • Yesaya 5:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Tsopano amuna inu, ndikuuzani zimene ndichite ndi munda wanga wa mpesa: Ndichotsa zomera zimene zinali ngati mpanda wa mundawo,+ ndipo ndiutentha.+ Ndigumula mpanda wake wamiyala ndipo mundawo udzangokhala malo oti azipondapondapo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena