Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Chotero anandiuza kuti: “Anthu otsala amene ali m’chigawo,*+ amene anathawa ku ukapolo, ali pamavuto aakulu+ ndipo akunyozedwa.+ Nawonso mpanda+ wa Yerusalemu unagwa ndipo zipata+ zake zinatenthedwa ndi moto.”

  • Yeremiya 24:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndidzawasandutsa chinthu chimene maufumu onse a padziko lapansi adzanthunthumira nacho, chifukwa cha masoka aakulu amene ndidzawagwetsera.+ Anthu a mitundu ina adzawatonza, kuwayesa chosereula, kuwanyoza+ ndipo adzakhala otembereredwa+ kulikonse kumene ndidzawabalalitsirako.+

  • Ezekieli 5:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “‘Iweyo ndidzakusandutsa malo abwinja. Ndidzakusandutsanso chitonzo pakati pa mitundu yokuzungulira ndi pamaso pa munthu aliyense wodutsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena