1 Mafumu 8:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Mukhululukire+ anthu anu amene anakuchimwirani.+ Muwakhululukirenso chifukwa cha malamulo anu onse amene anaphwanya,+ komanso owagwirawo akamawaona azikhudzidwa mtima+ ndi kuwachitira chisoni,
50 Mukhululukire+ anthu anu amene anakuchimwirani.+ Muwakhululukirenso chifukwa cha malamulo anu onse amene anaphwanya,+ komanso owagwirawo akamawaona azikhudzidwa mtima+ ndi kuwachitira chisoni,