Nehemiya 9:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Onani, lero ife ndife akapolo.+ Ndife akapolo m’dziko limene munapatsa makolo athu kuti adye zipatso zake ndi zinthu zake zabwino.+
36 Onani, lero ife ndife akapolo.+ Ndife akapolo m’dziko limene munapatsa makolo athu kuti adye zipatso zake ndi zinthu zake zabwino.+