Yesaya 58:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndimafunanso kuti muzigawira chakudya chanu anthu anjala,+ ndiponso kuti muziitanira m’nyumba zanu anthu osautsika ndi osowa pokhala.+ Ndimafuna kuti mukaona munthu wosavala muzimuveka+ ndiponso kuti musamadzibise kwa abale anu.+ Mateyu 25:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndinali wamaliseche+ koma inu munandiveka. Ndinadwala koma inu munandisamalira. Ndinali m’ndende+ koma inu munabwera kudzandiona.’ Luka 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Poyankha iye anali kuwauza kuti: “Munthu amene ali ndi malaya awiri amkati agawireko munthu amene alibiretu. Amenenso ali ndi chakudya achite chimodzimodzi.”+ Yakobo 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ngati m’bale kapena mlongo ali waumphawi ndipo alibe chakudya chokwanira pa tsikulo,+
7 Ndimafunanso kuti muzigawira chakudya chanu anthu anjala,+ ndiponso kuti muziitanira m’nyumba zanu anthu osautsika ndi osowa pokhala.+ Ndimafuna kuti mukaona munthu wosavala muzimuveka+ ndiponso kuti musamadzibise kwa abale anu.+
36 Ndinali wamaliseche+ koma inu munandiveka. Ndinadwala koma inu munandisamalira. Ndinali m’ndende+ koma inu munabwera kudzandiona.’
11 Poyankha iye anali kuwauza kuti: “Munthu amene ali ndi malaya awiri amkati agawireko munthu amene alibiretu. Amenenso ali ndi chakudya achite chimodzimodzi.”+