2 Iyeyu anali wopembedza+ ndi woopa+ Mulungu pamodzi ndi banja lake lonse. Anali kupatsa anthu mphatso zambiri zachifundo+ ndipo anali kupemphera kwa Mulungu nthawi zonse.+
17 Koma aliyense amene ali ndi zinthu zofunika pa moyo,+ n’kuona m’bale wake zikumusowa,+ koma osamusonyeza m’bale wakeyo chifundo chachikulu,+ kodi munthu ameneyu amakonda Mulungu?+