2 Akorinto 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zili choncho chifukwa utumiki wothandiza anthu umenewu si kuti ukungopatsa oyerawo zinthu zochuluka zimene akufunikira,+ koma ukuchititsanso anthu ambiri kupereka mapemphero ochuluka oyamika Mulungu.
12 Zili choncho chifukwa utumiki wothandiza anthu umenewu si kuti ukungopatsa oyerawo zinthu zochuluka zimene akufunikira,+ koma ukuchititsanso anthu ambiri kupereka mapemphero ochuluka oyamika Mulungu.