Mateyu 28:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho pitani mukaphunzitse anthu a mitundu yonse+ kuti akhale ophunzira anga.+ Muziwabatiza+ m’dzina la Atate,+ ndi la Mwana,+ ndi la mzimu woyera,+ Tito 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mawu amenewa ndi oona,+ ndipo ndikufuna kuti nthawi zonse uzinena zinthu zimenezi motsindika, kuti amene akukhulupirira Mulungu nthawi zonse aziganiza za mmene angapitirizire kuchita ntchito zabwino.+ Zinthu izi n’zabwino ndi zothandiza kwa anthu.
19 Choncho pitani mukaphunzitse anthu a mitundu yonse+ kuti akhale ophunzira anga.+ Muziwabatiza+ m’dzina la Atate,+ ndi la Mwana,+ ndi la mzimu woyera,+
8 Mawu amenewa ndi oona,+ ndipo ndikufuna kuti nthawi zonse uzinena zinthu zimenezi motsindika, kuti amene akukhulupirira Mulungu nthawi zonse aziganiza za mmene angapitirizire kuchita ntchito zabwino.+ Zinthu izi n’zabwino ndi zothandiza kwa anthu.