38 Petulo anawayankha kuti: “Lapani,+ ndipo aliyense wa inu abatizidwe+ m’dzina+ la Yesu Khristu kuti machimo anu akhululukidwe.+ Mukatero mudzalandira mphatso yaulere+ ya mzimu woyera.
12 Koma iwo atakhulupirira Filipo, amene anali kulengeza uthenga wabwino wonena za ufumu wa Mulungu+ ndi za dzina la Yesu Khristu, anabatizidwa, amuna ndi akazi omwe.+