-
2 Akorinto 8:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Koma ndikufuna kuti zinthu zambiri zimene muli nazo zithandize pa zimene iwowo alibe, ndipo zambiri zimene iwowo ali nazo zithandize pa zimene inuyo mulibe, kuti pakhale kufanana.
-