2 Akorinto 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma ndikufuna kuti zochuluka zimene muli nazo zithandizire pa zimene iwowo akusowa, ndipo zochuluka zimene iwowo ali nazo zithandizire pa zimene inuyo mukusowa, kuti pakhale kufanana.+ 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:14 Kodi Zopereka Zanu Zimagwiritsidwa Ntchito Bwanji?, article 5 Nsanja ya Olonda,1/15/1992, tsa. 17
14 Koma ndikufuna kuti zochuluka zimene muli nazo zithandizire pa zimene iwowo akusowa, ndipo zochuluka zimene iwowo ali nazo zithandizire pa zimene inuyo mukusowa, kuti pakhale kufanana.+
8:14 Kodi Zopereka Zanu Zimagwiritsidwa Ntchito Bwanji?, article 5 Nsanja ya Olonda,1/15/1992, tsa. 17