Yesaya 58:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndimafunanso kuti muzigawira chakudya chanu anthu anjala,+ ndiponso kuti muziitanira m’nyumba zanu anthu osautsika ndi osowa pokhala.+ Ndimafuna kuti mukaona munthu wosavala muzimuveka+ ndiponso kuti musamadzibise kwa abale anu.+ 1 Yohane 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ngati wina amanena kuti: “Ndimakonda Mulungu,” koma amadana ndi m’bale wake, ndiye kuti ndi wabodza.+ Pakuti amene sakonda m’bale wake+ amene amamuona, sangakonde Mulungu amene sanamuonepo.+
7 Ndimafunanso kuti muzigawira chakudya chanu anthu anjala,+ ndiponso kuti muziitanira m’nyumba zanu anthu osautsika ndi osowa pokhala.+ Ndimafuna kuti mukaona munthu wosavala muzimuveka+ ndiponso kuti musamadzibise kwa abale anu.+
20 Ngati wina amanena kuti: “Ndimakonda Mulungu,” koma amadana ndi m’bale wake, ndiye kuti ndi wabodza.+ Pakuti amene sakonda m’bale wake+ amene amamuona, sangakonde Mulungu amene sanamuonepo.+