Mateyu 25:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Koma poyankha mfumuyo+ idzawauza kuti, ‘Ndithu ndikukuuzani, Pa mlingo umene munachitira zimenezo mmodzi wa abale+ anga aang’ono+ awa, munachitira ine amene.’+ Maliko 9:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Chifukwa aliyense wokupatsani kapu+ ya madzi akumwa chifukwa chakuti ndinu ake a Khristu,+ ndithu ndikukuuzani, ameneyo mphoto yake sidzatayika ayi. Aheberi 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti Mulungu si wosalungama woti angaiwale ntchito yanu ndi chikondi chimene munachisonyeza pa dzina lake,+ mwa kutumikira oyera+ ndipo mukupitiriza kuwatumikira.
40 Koma poyankha mfumuyo+ idzawauza kuti, ‘Ndithu ndikukuuzani, Pa mlingo umene munachitira zimenezo mmodzi wa abale+ anga aang’ono+ awa, munachitira ine amene.’+
41 Chifukwa aliyense wokupatsani kapu+ ya madzi akumwa chifukwa chakuti ndinu ake a Khristu,+ ndithu ndikukuuzani, ameneyo mphoto yake sidzatayika ayi.
10 Pakuti Mulungu si wosalungama woti angaiwale ntchito yanu ndi chikondi chimene munachisonyeza pa dzina lake,+ mwa kutumikira oyera+ ndipo mukupitiriza kuwatumikira.