Mateyu 10:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Aliyense wopatsa mmodzi wa tiana iti ngakhale madzi ozizira okha mʼkapu kuti amwe chifukwa ndi wophunzira wanga, ndithu ndikukuuzani, ameneyo mphoto yake sidzatayika ngakhale pangʼono.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:42 Nsanja ya Olonda,1/1/1988, ptsa. 23-24
42 Aliyense wopatsa mmodzi wa tiana iti ngakhale madzi ozizira okha mʼkapu kuti amwe chifukwa ndi wophunzira wanga, ndithu ndikukuuzani, ameneyo mphoto yake sidzatayika ngakhale pangʼono.”+