1 Timoteyo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndithu, cholinga chokulamulira zimenezi n’chakuti tikhale ndi chikondi+ chochokera mumtima woyera,+ m’chikumbumtima chabwino,+ ndiponso m’chikhulupiriro chopanda chinyengo.+ 1 Timoteyo 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chifukwa chopereka malangizo awa kwa abale, udzakhala mtumiki wabwino wa Khristu Yesu. Ndipo udzakula bwino ndi mawu a chikhulupiriro ndiponso chiphunzitso chabwino+ chimene wachitsatira mosamala.+
5 Ndithu, cholinga chokulamulira zimenezi n’chakuti tikhale ndi chikondi+ chochokera mumtima woyera,+ m’chikumbumtima chabwino,+ ndiponso m’chikhulupiriro chopanda chinyengo.+
6 Chifukwa chopereka malangizo awa kwa abale, udzakhala mtumiki wabwino wa Khristu Yesu. Ndipo udzakula bwino ndi mawu a chikhulupiriro ndiponso chiphunzitso chabwino+ chimene wachitsatira mosamala.+