Yobu 28:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno anauza munthu kuti,‘Tamvera, kuopa Yehova ndiko nzeru,+Ndipo kupatuka pa choipa ndiko kumvetsa zinthu.’”+ Salimo 111:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chiyambi cha nzeru ndicho kuopa Yehova.+ ש [Sin]Onse otsatira malamulo a Mulungu ndi ozindikira.+ ת [Taw]Iye ayenera kutamandidwa mpaka muyaya.+ Miyambo 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kuopa Yehova ndiko chiyambi cha kudziwa zinthu.+ Nzeru ndi malangizo zimanyozedwa ndi zitsiru.*+ Miyambo 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso pakamwa ponena zopotoka.+
28 Ndiyeno anauza munthu kuti,‘Tamvera, kuopa Yehova ndiko nzeru,+Ndipo kupatuka pa choipa ndiko kumvetsa zinthu.’”+
10 Chiyambi cha nzeru ndicho kuopa Yehova.+ ש [Sin]Onse otsatira malamulo a Mulungu ndi ozindikira.+ ת [Taw]Iye ayenera kutamandidwa mpaka muyaya.+
13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso pakamwa ponena zopotoka.+